Troy Mob - Magetsi Azima

Troy Mob – Magetsi Azima

Music video by Troy Mob performing Magetsi Azima (Official Music Video). 2025 MOB Sound, distributed under Paradise Music Company & SIG Media.

Lyrics:

Kenny run it up

Magetsi azima
Nane ndipange zothima
Ndibwera mochedwa osasunga nsima
Ndivaye Paris nkaone ana akuvina

Magetsi azima
Nane ndipange zothima
Ndibwera mochedwa osasunga nsima
Ndivaye Paris nkaone ana akuvina

Undipeza m’munda nsakulima
Ma brandy nkagula pa Ema
Kukhala high pa phiri no Kina
Khutu la nkazi wako ndine m’matsina
Mwana sangandipake ine mimba
Ndungotchukabe ngati Gijima
Kunamizira ngati satimva
Koma sangabayite ndi Sativa
N’funa ngati chi Vanessa Dimasi
Chizivalako anga ma slippers
Tisakwiye ndayin’galura sibasi
Akhale oti sanadyeko T-kas
Ndungodabwa nazo zuchitikazi
Angopenga ndi trapper kuchikazi
Malaya alije mbwe ma set mayne
Fashion killer akuvala tetema
Pa ground pa man pachema
Chamba chotsala chonse nde tabema
Tungozimva udolo nde tabeba
Sangavunge beef ali ndi matemba
Kuyimba ngati ndili ndi matenda
Osakwiya nkazi wako tikatenga
Amangofuna yama nails ndi carpenter
Iwe umapala banja la ma carpenter

Gijima
Gijima
Gijima
Ndungotchukabe ngati Gijima
Gijima
Gijima
Gijima
Ndungotchukabe ngati Gijima

Magetsi azima
Nane ndipange zothima
Ndibwera mochedwa osasunga nsima
Ndivaye Paris nkaone ana akuvina

Magetsi azima
Nane ndipange zothima
Ndibwera mochedwa osasunga nsima
Ndivaye Paris nkaone ana akuvina

Leave a Reply

Back To Top